Ekisodo 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+ Salimo 72:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adalitsike Yehova Mulungu, Mulungu wa Isiraeli,+Iye yekha amene akuchita ntchito zodabwitsa.+ Salimo 77:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu ndinu Mulungu woona amene mukuchita zodabwitsa.+Mphamvu zanu mwazidziwikitsa pakati pa mitundu ya anthu.+ Danieli 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye amapulumutsa ndi kulanditsa anthu ake,+ ndipo amachita zizindikiro komanso zinthu zodabwitsa kumwamba+ ndi padziko lapansi,+ moti wapulumutsa Danieli kwa mikango.”
11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+
14 Inu ndinu Mulungu woona amene mukuchita zodabwitsa.+Mphamvu zanu mwazidziwikitsa pakati pa mitundu ya anthu.+
27 Iye amapulumutsa ndi kulanditsa anthu ake,+ ndipo amachita zizindikiro komanso zinthu zodabwitsa kumwamba+ ndi padziko lapansi,+ moti wapulumutsa Danieli kwa mikango.”