Yeremiya 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu munachita zizindikiro ndi zozizwitsa m’dziko la Iguputo. Zimene munachitazo zikudziwikabe mpaka pano mu Isiraeli ndiponso pakati pa anthu onse.+ Munachita zimenezo kuti mudzipangire dzina mofanana ndi zimene mukufuna kuchita posachedwapa.+ Danieli 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zizindikiro zake n’zazikulu ndipo zodabwitsa zake n’zamphamvu.+ Ufumu wake udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo ulamuliro wake udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+ Aheberi 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mulungu nayenso anachitira umboni za chipulumutsocho ndi zizindikiro, zinthu zodabwitsa, ntchito zamphamvu zosiyanasiyana+ komanso mwa kupereka mphatso zosiyanasiyana+ za mzimu woyera malinga ndi chifuniro chake.+
20 Inu munachita zizindikiro ndi zozizwitsa m’dziko la Iguputo. Zimene munachitazo zikudziwikabe mpaka pano mu Isiraeli ndiponso pakati pa anthu onse.+ Munachita zimenezo kuti mudzipangire dzina mofanana ndi zimene mukufuna kuchita posachedwapa.+
3 Zizindikiro zake n’zazikulu ndipo zodabwitsa zake n’zamphamvu.+ Ufumu wake udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo ulamuliro wake udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
4 Mulungu nayenso anachitira umboni za chipulumutsocho ndi zizindikiro, zinthu zodabwitsa, ntchito zamphamvu zosiyanasiyana+ komanso mwa kupereka mphatso zosiyanasiyana+ za mzimu woyera malinga ndi chifuniro chake.+