Salimo 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova ndi Mfumu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+Mitundu yatheratu padziko lapansi.+ Salimo 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wakhala pampando wake wachifumu pamwamba pa chigumula,*+Ndipo Yehova ndi mfumu mpaka kalekale.+ Salimo 66:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye akulamulira ndi mphamvu zake mpaka kalekale.+Maso ake akuyang’anitsitsa mitundu ya anthu.+Koma anthu oumitsa khosi asadzikweze.+ [Seʹlah.] Salimo 90:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mapiri asanabadwe,+Kapena musanakhazikitse dziko lapansi+ ndi malo okhalapo anthu,*+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+ Yeremiya 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi.+ Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu mpaka kalekale.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka ndi mkwiyo wake,+ ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzalimbe pamene iye akuidzudzula.+
10 Yehova wakhala pampando wake wachifumu pamwamba pa chigumula,*+Ndipo Yehova ndi mfumu mpaka kalekale.+
7 Iye akulamulira ndi mphamvu zake mpaka kalekale.+Maso ake akuyang’anitsitsa mitundu ya anthu.+Koma anthu oumitsa khosi asadzikweze.+ [Seʹlah.]
2 Mapiri asanabadwe,+Kapena musanakhazikitse dziko lapansi+ ndi malo okhalapo anthu,*+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+
10 Koma Yehova ndi Mulungu woonadi.+ Iye ndi Mulungu wamoyo+ ndipo ndi Mfumu mpaka kalekale.+ Dziko lapansi lidzagwedezeka ndi mkwiyo wake,+ ndipo palibe mitundu ya anthu imene idzalimbe pamene iye akuidzudzula.+