Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iye amadzutsa wonyozeka, kumuchotsa pafumbi.+

      Amachotsa osauka padzala,+

      Kuti awakhazike pakati pa anthu olemekezeka,+ ndipo amawapatsa mpando wachifumu waulemerero.+

      Pakuti michirikizo ya dziko lapansi ndi ya Yehova,+

      Ndipo anakhazika dziko lapansi pamichirikizo imeneyo.

  • 1 Mbiri 16:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Njenjemerani ndi mantha* pamaso pake, inu anthu nonse okhala padziko lapansi!

      Ndiponso dziko lapansi ndi lokhazikika,

      Silidzagwedezeka ku nthawi zonse.+

  • Salimo 89:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kumwamba ndi kwanu,+ dziko lapansi nalonso ndi lanu.+

      Nthaka ya dziko lapansi ndiponso zinthu zimene zili mmenemo+ munazipanga ndinu.+

  • Yeremiya 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mulungu woona ndi amene anapanga dziko lapansi ndi mphamvu zake,+ amene mwanzeru zake+ anakhazikitsa dziko limene anthu amakhalamo. Iye ndi amenenso anayala kumwamba mwa kuzindikira kwake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena