Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Pa chiyambi,+ Mulungu+ analenga+ kumwamba ndi dziko lapansi.+

  • Yobu 38:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Kodi unali kuti pamene ndinkaika maziko a dziko lapansi?+

      Ndiuze ngati uli womvetsa zinthu.

  • Salimo 89:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kumwamba ndi kwanu,+ dziko lapansi nalonso ndi lanu.+

      Nthaka ya dziko lapansi ndiponso zinthu zimene zili mmenemo+ munazipanga ndinu.+

  • Yesaya 40:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Kodi iwe sukudziwa kapena kodi sunamve?+ Yehova, Mlengi wa malekezero a dziko lapansi, ndiye Mulungu mpaka kalekale.+ Iye satopa kapena kufooka.+ Palibe amene angadziwe zimene iyeyo amazimvetsa.+

  • Yeremiya 51:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mulungu woona ndi amene anapanga dziko lapansi ndi mphamvu zake,+ amene mwanzeru+ zake anakhazikitsa dziko+ limene anthu amakhalamo. Iye ndi amenenso anayala kumwamba mwa kuzindikira kwake.+

  • Machitidwe 14:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 kuti: “Anthu inu, mukuchitiranji zimenezi? Ifenso ndife anthu+ okhala ndi zofooka+ ngati inu nomwe, ndipo tikulengeza uthenga wabwino kwa inu. Tikuchita izi kuti musiye zachabechabe zimenezi+ ndi kutembenukira kwa Mulungu wamoyo,+ amene anapanga kumwamba,+ dziko lapansi, nyanja ndi zonse zokhala mmenemo.

  • Chivumbulutso 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena