Salimo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka ndi yake pamodzi ndi onse okhala panthakapo.+ Salimo 50:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale nditakhala ndi njala, sindingakuuze,Pakuti dziko lonse+ ndiponso zonse za mmenemo ndi zanga.+
24 Dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka ndi yake pamodzi ndi onse okhala panthakapo.+
12 Ngakhale nditakhala ndi njala, sindingakuuze,Pakuti dziko lonse+ ndiponso zonse za mmenemo ndi zanga.+