Salimo 89:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumwamba ndi kwanu,+ dziko lapansi nalonso ndi lanu.+Nthaka ya dziko lapansi ndiponso zinthu zimene zili mmenemo+ munazipanga ndinu.+ Salimo 98:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nyanja ndi zonse zili mmenemo zichite mkokomo,+Chimodzimodzinso mtunda ndi zonse zokhala kumeneko.+
11 Kumwamba ndi kwanu,+ dziko lapansi nalonso ndi lanu.+Nthaka ya dziko lapansi ndiponso zinthu zimene zili mmenemo+ munazipanga ndinu.+
7 Nyanja ndi zonse zili mmenemo zichite mkokomo,+Chimodzimodzinso mtunda ndi zonse zokhala kumeneko.+