Mateyu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Momwemonso, onetsani kuwala+ kwanu pamaso pa anthu, kuti aone ntchito zanu zabwino+ ndi kuti alemekeze+ Atate wanu wakumwamba. Chivumbulutso 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anali kunena mofuula kuti: “Opani Mulungu+ ndi kumupatsa ulemerero,+ chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Chotero lambirani Iye amene anapanga+ kumwamba, dziko lapansi, nyanja, ndi akasupe amadzi.”+
16 Momwemonso, onetsani kuwala+ kwanu pamaso pa anthu, kuti aone ntchito zanu zabwino+ ndi kuti alemekeze+ Atate wanu wakumwamba.
7 Iye anali kunena mofuula kuti: “Opani Mulungu+ ndi kumupatsa ulemerero,+ chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Chotero lambirani Iye amene anapanga+ kumwamba, dziko lapansi, nyanja, ndi akasupe amadzi.”+