Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 19:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+

      Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+

  • Aroma 11:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Chifukwa zinthu zonse zimachokera kwa iye ndipo iye ndi amene anazipanga ndiponso ndi zake.+ Ulemerero ukhale wake kwamuyaya.+ Ame.

  • Yuda 25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 kwa iyeyo, Mulungu yekhayo amenenso ndi Mpulumutsi wathu+ mwa Yesu Khristu+ Ambuye wathu, kukhale ulemerero,+ ukulu, mphamvu+ ndi ulamuliro,+ kuchokera kalekale+ kufikira panopa, mpaka ku nthawi yonse yomka muyaya.+ Ame.+

  • Chivumbulutso 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Nthawi zonse zamoyozo zikamapereka ulemerero, ndi ulemu, ndiponso zikamayamikira+ Wokhala pampando wachifumuyo,+ Iye amene adzakhalabe ndi moyo kwamuyaya,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena