Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 8:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Ndikayang’ana kumwamba, ntchito ya zala zanu,+

      Mwezi ndi nyenyezi zimene munapanga,+

  • Salimo 69:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Kumwamba ndi dziko lapansi zimutamande,+

      Chimodzimodzinso nyanja ndi chilichonse choyenda mmenemo.+

  • Salimo 115:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Inu ndinu amene mwadalitsidwa ndi Yehova,+

      Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi.+

  • Salimo 148:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mutamandeni, inu dzuwa ndi mwezi.+

      Mutamandeni, inu nyenyezi zonse zowala.+

  • Yesaya 40:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pali Winawake amene amakhala pamwamba pa dziko lapansi lozungulira,+ limene okhalamo ake ali ngati ziwala. Iye anayala kumwamba ngati nsalu yopyapyala, ndipo anakutambasula ngati hema wokhalamo.+

  • Aroma 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Chilengedwere dziko kupita m’tsogolo,+ makhalidwe a Mulungu osaoneka+ ndi maso akuonekera bwino. Makhalidwe a Mulungu amenewa, ngakhalenso mphamvu zake zosatha+ ndiponso Umulungu+ wake, zikuonekera m’zinthu zimene anapanga+ moti anthuwo alibenso chifukwa chomveka chosakhulupirira kuti kuli Mulungu.+

  • 1 Akorinto 15:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Palinso matupi akumwamba,+ ndi matupi+ apadziko lapansi, koma ulemerero+ wa matupi akumwamba ndi wina, ndipo ulemerero wa matupi apadziko lapansi ndi winanso.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena