Yeremiya 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mulungu woona ndi amene anapanga dziko lapansi ndi mphamvu zake,+ amene mwanzeru zake+ anakhazikitsa dziko limene anthu amakhalamo. Iye ndi amenenso anayala kumwamba mwa kuzindikira kwake.+ 2 Petulo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti Mulungu, mwa mphamvu yake, watipatsa kwaulere zinthu zonse zofunika kuti munthu akhale moyo+ wodzipereka kwa Mulungu.+ Talandira zinthu zimenezi kudzera mwa kudziwa molondola za iye amene anatiitana,+ kudzera mu ulemerero+ ndi ubwino wake.
12 Mulungu woona ndi amene anapanga dziko lapansi ndi mphamvu zake,+ amene mwanzeru zake+ anakhazikitsa dziko limene anthu amakhalamo. Iye ndi amenenso anayala kumwamba mwa kuzindikira kwake.+
3 Pakuti Mulungu, mwa mphamvu yake, watipatsa kwaulere zinthu zonse zofunika kuti munthu akhale moyo+ wodzipereka kwa Mulungu.+ Talandira zinthu zimenezi kudzera mwa kudziwa molondola za iye amene anatiitana,+ kudzera mu ulemerero+ ndi ubwino wake.