Genesis 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Motero Mulungu anapanga zounikira zikuluzikulu ziwiri. Chounikira chokulirapo anachipanga kuti chilamulire usana, ndi chocheperapo kuti chilamulire usiku, komanso nyenyezi.+ Salimo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+ Salimo 136:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amenenso anapanga dzuwa kuti lizilamulira masana:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
16 Motero Mulungu anapanga zounikira zikuluzikulu ziwiri. Chounikira chokulirapo anachipanga kuti chilamulire usana, ndi chocheperapo kuti chilamulire usiku, komanso nyenyezi.+
19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+
8 Amenenso anapanga dzuwa kuti lizilamulira masana:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+