Genesis 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mulungu tsopano anati: “Pakhale mlengalenga+ pakati pa madzi, ndiponso pakhale cholekanitsa pakati pa madzi ndi madzi.”+ Salimo 150:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 150 Tamandani Ya, anthu inu!+Tamandani Mulungu m’malo ake oyera.+Mutamandeni m’mlengalenga mmene mumasonyeza mphamvu zake.+ Chivumbulutso 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+
6 Mulungu tsopano anati: “Pakhale mlengalenga+ pakati pa madzi, ndiponso pakhale cholekanitsa pakati pa madzi ndi madzi.”+
150 Tamandani Ya, anthu inu!+Tamandani Mulungu m’malo ake oyera.+Mutamandeni m’mlengalenga mmene mumasonyeza mphamvu zake.+
11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+