Genesis 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mulungu tsopano anati: “Pakhale mlengalenga+ pakati pa madzi, ndiponso pakhale cholekanitsa pakati pa madzi ndi madzi.”+ Salimo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+ Danieli 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Anthu ozindikira adzawala ngati kuwala kwa kuthambo.+ Ndipo amene akuthandiza anthu ambiri kukhala olungama+ adzawala ngati nyenyezi mpaka kalekale, inde, kwamuyaya.
6 Mulungu tsopano anati: “Pakhale mlengalenga+ pakati pa madzi, ndiponso pakhale cholekanitsa pakati pa madzi ndi madzi.”+
19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+
3 “Anthu ozindikira adzawala ngati kuwala kwa kuthambo.+ Ndipo amene akuthandiza anthu ambiri kukhala olungama+ adzawala ngati nyenyezi mpaka kalekale, inde, kwamuyaya.