Salimo 33:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anasonkhanitsa madzi a m’nyanja ngati wachita kuwatchinga ndi khoma,+Anaika madzi amphamvu m’nyumba zosungiramo zinthu. 2 Petulo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu amenewa, mwa kufuna kwawo amalephera kuzindikira mfundo iyi yakuti, panali kumwamba+ kuchokera kalekale, ndipo mwa mawu a Mulungu, dziko lapansi linali loumbika motsendereka pamwamba pa madzi+ ndi pakati pa madzi,+
7 Anasonkhanitsa madzi a m’nyanja ngati wachita kuwatchinga ndi khoma,+Anaika madzi amphamvu m’nyumba zosungiramo zinthu.
5 Anthu amenewa, mwa kufuna kwawo amalephera kuzindikira mfundo iyi yakuti, panali kumwamba+ kuchokera kalekale, ndipo mwa mawu a Mulungu, dziko lapansi linali loumbika motsendereka pamwamba pa madzi+ ndi pakati pa madzi,+