-
Yobu 38:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndani anatseka nyanja ndi zitseko,+
Imene inayamba kuyenda ngati kuti ikutumphuka m’mimba?
-
Yeremiya 5:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 ‘Kodi simundiopa?’+ watero Yehova. ‘Kapena kodi simukumva ululu waukulu chifukwa cha ine?+ Ine ndinaika mchenga kukhala malire a nyanja, malire okhalapo mpaka kalekale amene nyanjayo singadutse. Ngakhale kuti mafunde amawinduka sangadutse malirewo ndipo ngakhale amachita phokoso sangawapitirire.+
-
-
-