Yobu 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako ndinaiuza kuti, ‘Ukhoza kufika apa, koma usapitirirepo,+Ndipo mafunde ako aatali azilekezera pamenepa.’+ Salimo 104:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kupita kumalo amene munawakonzera.Mapiri anakwera,+Zigwa zinatsika. Salimo 136:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yamikani woyala dziko lapansi pamwamba pa madzi:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
11 Kenako ndinaiuza kuti, ‘Ukhoza kufika apa, koma usapitirirepo,+Ndipo mafunde ako aatali azilekezera pamenepa.’+
6 Yamikani woyala dziko lapansi pamwamba pa madzi:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+