Salimo 33:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anasonkhanitsa madzi a m’nyanja ngati wachita kuwatchinga ndi khoma,+Anaika madzi amphamvu m’nyumba zosungiramo zinthu. Miyambo 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 pamene anaikira nyanja lamulo lake lakuti madzi ake asapitirire pamene anawalamula,+ pamene anakhazikitsa maziko a dziko lapansi,+ Machitidwe 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu+ mokweza mawu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa,+ Inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zokhala mmenemo.+
7 Anasonkhanitsa madzi a m’nyanja ngati wachita kuwatchinga ndi khoma,+Anaika madzi amphamvu m’nyumba zosungiramo zinthu.
29 pamene anaikira nyanja lamulo lake lakuti madzi ake asapitirire pamene anawalamula,+ pamene anakhazikitsa maziko a dziko lapansi,+
24 Atamva zimenezi, onse pamodzi anafuula kwa Mulungu+ mokweza mawu kuti: “Ambuye Wamkulu Koposa,+ Inu ndi amene munapanga kumwamba ndi dziko lapansi, nyanja ndi zonse zokhala mmenemo.+