Yobu 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anaika malire ozungulira pamwamba pa madzi,+Kumene kuwala kumakathera mu mdima. Yobu 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako ndinaiuza kuti, ‘Ukhoza kufika apa, koma usapitirirepo,+Ndipo mafunde ako aatali azilekezera pamenepa.’+ Salimo 33:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anasonkhanitsa madzi a m’nyanja ngati wachita kuwatchinga ndi khoma,+Anaika madzi amphamvu m’nyumba zosungiramo zinthu. Salimo 104:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munawaikira malire kuti asapitirire malirewo,+Kuti asamizenso dziko lapansi.+ Miyambo 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 pamene anaikira nyanja lamulo lake lakuti madzi ake asapitirire pamene anawalamula,+ pamene anakhazikitsa maziko a dziko lapansi,+
11 Kenako ndinaiuza kuti, ‘Ukhoza kufika apa, koma usapitirirepo,+Ndipo mafunde ako aatali azilekezera pamenepa.’+
7 Anasonkhanitsa madzi a m’nyanja ngati wachita kuwatchinga ndi khoma,+Anaika madzi amphamvu m’nyumba zosungiramo zinthu.
29 pamene anaikira nyanja lamulo lake lakuti madzi ake asapitirire pamene anawalamula,+ pamene anakhazikitsa maziko a dziko lapansi,+