Genesis 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pangano limene ndikuchita nanu ndi ili: Zamoyo zonse sizidzawonongedwanso ndi madzi a chigumula, ndipo chigumula sichidzachitikanso n’kuwononga dziko lapansi.”+
11 Pangano limene ndikuchita nanu ndi ili: Zamoyo zonse sizidzawonongedwanso ndi madzi a chigumula, ndipo chigumula sichidzachitikanso n’kuwononga dziko lapansi.”+