Danieli 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anthu ozindikira+ pakati pa anthuwo adzathandiza anthu ambiri kumvetsa zinthu.+ Iwo adzapunthwa kwa kanthawi ndi lupanga ndi malawi a moto. Adzapunthwanso mwa kutengedwa ukapolo ndi kuwonongedwa kwa zinthu zawo.+ Mateyu 13:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pa nthawi imeneyo olungama adzawala+ kwambiri ngati dzuwa+ mu ufumu wa Atate wawo. Amene ali ndi makutu amve.+
33 Anthu ozindikira+ pakati pa anthuwo adzathandiza anthu ambiri kumvetsa zinthu.+ Iwo adzapunthwa kwa kanthawi ndi lupanga ndi malawi a moto. Adzapunthwanso mwa kutengedwa ukapolo ndi kuwonongedwa kwa zinthu zawo.+
43 Pa nthawi imeneyo olungama adzawala+ kwambiri ngati dzuwa+ mu ufumu wa Atate wawo. Amene ali ndi makutu amve.+