Oweruza 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Inu Yehova, adani anu onse afafanizidwe chimodzimodzi,+Ndipo okukondani inu+ akhale amphamvu ngati mmene dzuwa limakhalira.”+Choncho, dzikolo linakhala pa mtendere zaka 40.+ 2 Samueli 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ulamuliro wake umakhala ngati kuwala kwa m’mawa pamene dzuwa lawala,+M’mawa wopanda mitambo.Umakhala ngati msipu womera padziko mvula ikakata, dzuwa n’kuwala.’+
31 Inu Yehova, adani anu onse afafanizidwe chimodzimodzi,+Ndipo okukondani inu+ akhale amphamvu ngati mmene dzuwa limakhalira.”+Choncho, dzikolo linakhala pa mtendere zaka 40.+
4 Ulamuliro wake umakhala ngati kuwala kwa m’mawa pamene dzuwa lawala,+M’mawa wopanda mitambo.Umakhala ngati msipu womera padziko mvula ikakata, dzuwa n’kuwala.’+