Salimo 68:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Monga mmene mphepo imauluzira utsi, inunso muwauluze chimodzimodzi.+Ngati mmene phula limasungunukira chifukwa cha moto,+Anthu oipa awonongeke ndi kuchotsedwa pamaso pa Mulungu.+ Salimo 83:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani+ ndi Sisera.+Muwachitirenso zimene munachitira Yabini+ kuchigwa cha Kisoni.+ Salimo 92:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti taonani adani anu, inu Yehova!+Adani anu onse adzatha!+Anthu onse ochita zopweteka anzawo adzamwazikana.+
2 Monga mmene mphepo imauluzira utsi, inunso muwauluze chimodzimodzi.+Ngati mmene phula limasungunukira chifukwa cha moto,+Anthu oipa awonongeke ndi kuchotsedwa pamaso pa Mulungu.+
9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani+ ndi Sisera.+Muwachitirenso zimene munachitira Yabini+ kuchigwa cha Kisoni.+
9 Pakuti taonani adani anu, inu Yehova!+Adani anu onse adzatha!+Anthu onse ochita zopweteka anzawo adzamwazikana.+