Salimo 97:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapiri anasungunuka ngati phula chifukwa cha Yehova,+Chifukwa cha Ambuye wa dziko lonse lapansi.+ Mika 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mapiri asungunuka kumapazi ake+ ndipo zigwa zigawanika. Zonsezi zisungunuka ngati phula losungunuka ndi moto+ ndipo ziyenda ngati madzi othiridwa pamalo otsetsereka.
4 Mapiri asungunuka kumapazi ake+ ndipo zigwa zigawanika. Zonsezi zisungunuka ngati phula losungunuka ndi moto+ ndipo ziyenda ngati madzi othiridwa pamalo otsetsereka.