Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Mapiri anasungunuka ndi kuyenda ngati madzi, kuchoka pamaso pa Yehova,+

      Sinai+ uyu anayenda ngati madzi kuchoka pamaso pa Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli.+

  • Mika 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mapiri asungunuka kumapazi ake+ ndipo zigwa zigawanika. Zonsezi zisungunuka ngati phula losungunuka ndi moto+ ndipo ziyenda ngati madzi othiridwa pamalo otsetsereka.

  • Nahumu 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mapiri agwedezeka chifukwa cha iye ndipo zitunda zasungunuka.+

      Dziko lapansi, nthaka ndi zinthu zonse zokhala m’dzikomo zidzanjenjemera.+

  • Habakuku 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye anaima chilili kuti agwedeze dziko lapansi.+ Anayang’ana mitundu ya anthu ndipo mitunduyo inadumpha.+

      Mapiri amuyaya anaphwanyidwa.+ Zitunda zimene zidzakhalapo mpaka kalekale* zinawerama.+ Zimenezi ndi njira zake zakalekale.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena