Genesis 49:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Madalitso a bambo ako adzapambana madalitso a mapiri amene adzakhalapo mpaka kalekale.+ Adzapambananso ulemerero wa zitunda zosatha.+ Madalitsowo adzakhalabe pamutu pa Yosefe, paliwombo pa wosankhidwa pakati pa abale ake.+ Yesaya 54:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti mapiri akhoza kuchotsedwa, ndipo zitunda zikhoza kugwedezeka,+ koma kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachotsedwa kwa iwe,+ ndipo pangano langa la mtendere silidzagwedezeka,”+ watero Yehova, amene akukuchitira chifundo.+
26 Madalitso a bambo ako adzapambana madalitso a mapiri amene adzakhalapo mpaka kalekale.+ Adzapambananso ulemerero wa zitunda zosatha.+ Madalitsowo adzakhalabe pamutu pa Yosefe, paliwombo pa wosankhidwa pakati pa abale ake.+
10 Pakuti mapiri akhoza kuchotsedwa, ndipo zitunda zikhoza kugwedezeka,+ koma kukoma mtima kwanga kosatha sikudzachotsedwa kwa iwe,+ ndipo pangano langa la mtendere silidzagwedezeka,”+ watero Yehova, amene akukuchitira chifundo.+