Deuteronomo 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri za padziko lapansi, ndi chuma chake chonse,+Komanso movomerezedwa ndi Iye amene anaonekera m’chitsamba chaminga.+Zimenezi zikhale pamutu pa Yosefe,+Paliwombo pa munthu wopatulidwa pakati pa abale ake.+ Machitidwe 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+
16 Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri za padziko lapansi, ndi chuma chake chonse,+Komanso movomerezedwa ndi Iye amene anaonekera m’chitsamba chaminga.+Zimenezi zikhale pamutu pa Yosefe,+Paliwombo pa munthu wopatulidwa pakati pa abale ake.+
9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+