Ekisodo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova ataona kuti Mose wapatuka kuti akaonetsetse, nthawi yomweyo Mulungu anamuitana kuchokera pakatikati pa chitsamba chamingacho, kuti: “Mose! Mose!” ndipo iye anayankha kuti: “Ndili pano.”+ Machitidwe 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye m’malawi a moto pachitsamba chaminga+ m’chipululu, pafupi ndi phiri la Sinai.
4 Yehova ataona kuti Mose wapatuka kuti akaonetsetse, nthawi yomweyo Mulungu anamuitana kuchokera pakatikati pa chitsamba chamingacho, kuti: “Mose! Mose!” ndipo iye anayankha kuti: “Ndili pano.”+
30 “Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye m’malawi a moto pachitsamba chaminga+ m’chipululu, pafupi ndi phiri la Sinai.