Ekisodo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako mngelo wa Yehova anaonekera kwa iye pakati pa chitsamba chaminga+ chimene chinali kuyaka moto. Atachiyang’anitsitsa, anaona kuti chitsamba chamingacho chikuyaka, koma sichikupsa. Yesaya 63:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene iwo anali kuvutika m’masautso awo onse, iyenso anali kuvutika.+ Mthenga amene iye anawatumizira, anawapulumutsa.+ Chifukwa cha chikondi chake ndi chisoni chake, iye anawawombola.+ Anawakweza m’mwamba ndi kuwanyamula masiku onse akale.+
2 Kenako mngelo wa Yehova anaonekera kwa iye pakati pa chitsamba chaminga+ chimene chinali kuyaka moto. Atachiyang’anitsitsa, anaona kuti chitsamba chamingacho chikuyaka, koma sichikupsa.
9 Pamene iwo anali kuvutika m’masautso awo onse, iyenso anali kuvutika.+ Mthenga amene iye anawatumizira, anawapulumutsa.+ Chifukwa cha chikondi chake ndi chisoni chake, iye anawawombola.+ Anawakweza m’mwamba ndi kuwanyamula masiku onse akale.+