Deuteronomo 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri za padziko lapansi, ndi chuma chake chonse,+Komanso movomerezedwa ndi Iye amene anaonekera m’chitsamba chaminga.+Zimenezi zikhale pamutu pa Yosefe,+Paliwombo pa munthu wopatulidwa pakati pa abale ake.+ Machitidwe 7:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye m’malawi a moto pachitsamba chaminga+ m’chipululu, pafupi ndi phiri la Sinai.
16 Lidalitsidwe ndi zinthu zabwino kwambiri za padziko lapansi, ndi chuma chake chonse,+Komanso movomerezedwa ndi Iye amene anaonekera m’chitsamba chaminga.+Zimenezi zikhale pamutu pa Yosefe,+Paliwombo pa munthu wopatulidwa pakati pa abale ake.+
30 “Patapita zaka 40, mngelo anaonekera kwa iye m’malawi a moto pachitsamba chaminga+ m’chipululu, pafupi ndi phiri la Sinai.