Yesaya 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti Yehova adzachitira chifundo Yakobo+ ndipo adzasankhanso Isiraeli.+ Iye adzawapatsa mpumulo m’dziko lawo.+ Alendo adzakhala nawo limodzi ndipo adzadziphatika kunyumba ya Yakobo.+ Aefeso 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Mulungu, amene ndi wachifundo chochuluka,+ mwachikondi chake chachikulu chimene anatikonda nacho,+
14 Pakuti Yehova adzachitira chifundo Yakobo+ ndipo adzasankhanso Isiraeli.+ Iye adzawapatsa mpumulo m’dziko lawo.+ Alendo adzakhala nawo limodzi ndipo adzadziphatika kunyumba ya Yakobo.+
4 Koma Mulungu, amene ndi wachifundo chochuluka,+ mwachikondi chake chachikulu chimene anatikonda nacho,+