Aroma 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Mulungu akuonetsa chikondi chake+ kwa ife, moti pamene tinali ochimwa, Khristu anatifera.+ 1 Yohane 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mulungu anatisonyeza ife chikondi chake+ pakuti anatumiza m’dziko Mwana wake wobadwa yekha+ kuti tipeze moyo kudzera mwa iye.+ 1 Yohane 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma ife timasonyeza chikondi, chifukwa iye ndi amene anayamba kutikonda.+
9 Mulungu anatisonyeza ife chikondi chake+ pakuti anatumiza m’dziko Mwana wake wobadwa yekha+ kuti tipeze moyo kudzera mwa iye.+