Zekariya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Fuulanso kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Mizinda yanga idzasefukira ndi zinthu zabwino.+ Yehova adzamva chisoni chifukwa cha tsoka limene anagwetsera Ziyoni+ ndipo adzasankhanso Yerusalemu.”’”+ Aroma 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiye zili bwanji pamenepa? Chimene Aisiraeli akuchifunitsitsa sanachipeze,+ koma anthu osankhidwa+ ndi amene anachipeza. Enawo anaumitsa mitima yawo+
17 “Fuulanso kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Mizinda yanga idzasefukira ndi zinthu zabwino.+ Yehova adzamva chisoni chifukwa cha tsoka limene anagwetsera Ziyoni+ ndipo adzasankhanso Yerusalemu.”’”+
7 Ndiye zili bwanji pamenepa? Chimene Aisiraeli akuchifunitsitsa sanachipeze,+ koma anthu osankhidwa+ ndi amene anachipeza. Enawo anaumitsa mitima yawo+