Salimo 132:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wasankha Ziyoni,+Ndipo amafunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye amati:+ Zekariya 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako mngelo+ wa Yehova anauza Satana kuti: “Iwe Satana, Yehova akudzudzule!+ Yehova amene anasankha Yerusalemu akudzudzule!+ Kodi munthu uyu si chikuni chimene chaphulidwa pamoto msangamsanga?”+
2 Kenako mngelo+ wa Yehova anauza Satana kuti: “Iwe Satana, Yehova akudzudzule!+ Yehova amene anasankha Yerusalemu akudzudzule!+ Kodi munthu uyu si chikuni chimene chaphulidwa pamoto msangamsanga?”+