Salimo 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu inu, imbani nyimbo motsagana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda Yehova amene akukhala m’Ziyoni.+Fotokozani ntchito zake kwa mitundu ya anthu.+ Salimo 48:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munsanja zokhalamo za m’mudzimo, Mulungu wadziwika kuti ndi malo okwezeka ndiponso achitetezo.+ Salimo 74:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumbukirani anthu amene munawatenga kukhala anu kalelo,+Fuko limene munaliwombola monga cholowa chanu,+Ndi phiri la Ziyoni ili mmene inu mukukhala.+ Salimo 76:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malo ake opumulirako ali ku Salemu,+Malo ake okhalamo ali ku Ziyoni.+ Salimo 78:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Koma anasankha fuko la Yuda,+Phiri la Ziyoni limene analikonda.+ Salimo 135:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova amene akukhala ku Yerusalemu,+Atamandidwe mu Ziyoni.+Tamandani Ya, anthu inu!+ Aheberi 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma m’malomwake, inu mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda+ wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo miyandamiyanda,*+
11 Anthu inu, imbani nyimbo motsagana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda Yehova amene akukhala m’Ziyoni.+Fotokozani ntchito zake kwa mitundu ya anthu.+
2 Kumbukirani anthu amene munawatenga kukhala anu kalelo,+Fuko limene munaliwombola monga cholowa chanu,+Ndi phiri la Ziyoni ili mmene inu mukukhala.+
22 Koma m’malomwake, inu mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda+ wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo miyandamiyanda,*+