Salimo 66:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Bwerani anthu inu, kuti muone ntchito za Mulungu.+Zimene wachitira ana a anthu ndi zochititsa mantha.+ Salimo 96:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nenani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala mfumu.+Dziko lapansi nalonso lakhazikika moti silingagwedezeke.+Iye adzaweruzira mitundu ya anthu milandu yawo mwachilungamo.”+ Salimo 105:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 105 YAMIKANI Yehova, itanani pa dzina lake,+Lengezani zochita zake pakati pa mitundu ya anthu.+ Salimo 107:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iwo apereke nsembe zoyamikira,+Ndi kulengeza za ntchito zake ndi mfuu yachisangalalo.+ Yesaya 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’tsiku limenelo mudzanenadi kuti: “Yamikani Yehova anthu inu.+ Itanani pa dzina lake.+ Dziwitsani mitundu ya anthu zochita zake.+ Nenani kuti dzina lake n’lokwezeka.+
5 Bwerani anthu inu, kuti muone ntchito za Mulungu.+Zimene wachitira ana a anthu ndi zochititsa mantha.+
10 Nenani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala mfumu.+Dziko lapansi nalonso lakhazikika moti silingagwedezeke.+Iye adzaweruzira mitundu ya anthu milandu yawo mwachilungamo.”+
4 M’tsiku limenelo mudzanenadi kuti: “Yamikani Yehova anthu inu.+ Itanani pa dzina lake.+ Dziwitsani mitundu ya anthu zochita zake.+ Nenani kuti dzina lake n’lokwezeka.+