Salimo 105:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 105 Yamikani Yehova,+ itanani pa dzina lake,Dziwitsani mitundu ya anthu ntchito zake.+