Salimo 105:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 105 YAMIKANI Yehova, itanani pa dzina lake,+Lengezani zochita zake pakati pa mitundu ya anthu.+