Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 16:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 “Yamikani Yehova,+ anthu inu. Itanani pa dzina lake.+

      Dziwitsani mitundu ya anthu ntchito zake!+

  • Salimo 136:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 136 Yamikani Yehova anthu inu, pakuti iye ndi wabwino:+

      Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+

  • Yesaya 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 M’tsiku limenelo mudzanenadi kuti: “Yamikani Yehova anthu inu.+ Itanani pa dzina lake.+ Dziwitsani mitundu ya anthu zochita zake.+ Nenani kuti dzina lake n’lokwezeka.+

  • Yoweli 2:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ndiyeno aliyense woitana pa dzina la Yehova adzapulumuka,+ pakuti m’phiri la Ziyoni ndiponso mu Yerusalemu mudzakhala anthu opulumuka+ monga mmene Yehova ananenera. Amenewa ndi anthu amene Yehova akuwaitana.”+

  • Aroma 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pakuti “aliyense amene adzaitana pa dzina la Yehova* adzapulumuka.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena