Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Machitidwe 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo aliyense woitana pa dzina la Yehova adzapulumuka.”’+ Aroma 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti “aliyense amene adzaitana pa dzina la Yehova* adzapulumuka.”+