Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 33:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Iye atasautsika mumtima mwake chifukwa cha zimenezi,+ anakhazikitsa pansi mtima wa Yehova Mulungu wake+ ndipo anadzichepetsa+ kwambiri pamaso pa Mulungu wa makolo ake.

  • Salimo 77:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Pa tsiku la zowawa zanga ndafunafuna Yehova.+

      Ndakweza dzanja langa kumwamba usiku wonse, ndipo silinachite dzanzi.

      Koma sindinatonthozeke.+

  • Salimo 91:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+

      Ndidzakhala naye m’nthawi ya masautso.+

      Ndidzamupulumutsa ndi kumupatsa ulemerero.+

  • Luka 22:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Koma atazunzika koopsa mumtima mwake, anapitiriza kupemphera ndi mtima wonse+ ndipo thukuta lake linaoneka ngati madontho amagazi amene akugwera pansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena