Salimo 138:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndikakhala pa masautso, inu mudzandisunga wamoyo.+Mudzatambasula dzanja lanu chifukwa cha mkwiyo wa adani anga,+Ndipo dzanja lanu lamanja lidzandipulumutsa.+ Yesaya 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ukamadzadutsa pamadzi,+ ine ndidzakhala nawe.+ Ukamadzawoloka mitsinje, madzi sadzakumiza.+ Ukamadzayenda pamoto sudzapsa ndipo ngakhale lawi la moto silidzakuwaula.+
7 Ndikakhala pa masautso, inu mudzandisunga wamoyo.+Mudzatambasula dzanja lanu chifukwa cha mkwiyo wa adani anga,+Ndipo dzanja lanu lamanja lidzandipulumutsa.+
2 Ukamadzadutsa pamadzi,+ ine ndidzakhala nawe.+ Ukamadzawoloka mitsinje, madzi sadzakumiza.+ Ukamadzayenda pamoto sudzapsa ndipo ngakhale lawi la moto silidzakuwaula.+