Ekisodo 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma ana Aisiraeli anayenda panthaka youma pakati pa nyanja,+ ndipo madzi anaima ngati khoma kudzanja lawo lamanja ndi lamanzere.+ Yoswa 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Onyamula Likasawo atangofika kumtsinje wa Yorodano, n’kuponda madzi a m’mphepete mwa mtsinjewo (mtsinje wa Yorodano unali kusefukira+ nyengo yonse yokolola), Salimo 66:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwachititsa munthu wamba kutipondaponda.+Tadutsa pamoto ndi pamadzi,+Ndipo inu mwatipatsa mpumulo.+ Aheberi 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mwa chikhulupiriro, anthu a Mulunguwo anawoloka Nyanja Yofiira ngati kuti akudutsa pamtunda pouma,+ koma Aiguputo atalimba mtima ndi kulowa panyanjapo, nyanjayo inawamiza.+
29 Koma ana Aisiraeli anayenda panthaka youma pakati pa nyanja,+ ndipo madzi anaima ngati khoma kudzanja lawo lamanja ndi lamanzere.+
15 Onyamula Likasawo atangofika kumtsinje wa Yorodano, n’kuponda madzi a m’mphepete mwa mtsinjewo (mtsinje wa Yorodano unali kusefukira+ nyengo yonse yokolola),
12 Mwachititsa munthu wamba kutipondaponda.+Tadutsa pamoto ndi pamadzi,+Ndipo inu mwatipatsa mpumulo.+
29 Mwa chikhulupiriro, anthu a Mulunguwo anawoloka Nyanja Yofiira ngati kuti akudutsa pamtunda pouma,+ koma Aiguputo atalimba mtima ndi kulowa panyanjapo, nyanjayo inawamiza.+