Yoswa 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ansembe onyamula likasa+ la pangano la Yehova atatuluka pakati pa mtsinje wa Yorodano, ndipo mapazi+ awo ataponda kumtunda, madzi a mtsinjewo anayamba kubwerera mwakale, ndipo anasefukira+ mbali zonse ngati poyamba. 1 Mbiri 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Awa ndi amene anawoloka mtsinje wa Yorodano+ m’mwezi woyamba* pamene mtsinjewo unasefukira mbali zake zonse.+ Kenako anathamangitsira kum’mawa ndi kumadzulo anthu onse amene anali kukhala m’zigwa.
18 Ansembe onyamula likasa+ la pangano la Yehova atatuluka pakati pa mtsinje wa Yorodano, ndipo mapazi+ awo ataponda kumtunda, madzi a mtsinjewo anayamba kubwerera mwakale, ndipo anasefukira+ mbali zonse ngati poyamba.
15 Awa ndi amene anawoloka mtsinje wa Yorodano+ m’mwezi woyamba* pamene mtsinjewo unasefukira mbali zake zonse.+ Kenako anathamangitsira kum’mawa ndi kumadzulo anthu onse amene anali kukhala m’zigwa.