1 Mbiri 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Awa ndi amene anawoloka mtsinje wa Yorodano mʼmwezi woyamba* pamene mtsinjewo unasefukira. Ndipo anathamangitsira kumʼmawa ndi kumadzulo anthu onse amene ankakhala mʼzigwa.
15 Awa ndi amene anawoloka mtsinje wa Yorodano mʼmwezi woyamba* pamene mtsinjewo unasefukira. Ndipo anathamangitsira kumʼmawa ndi kumadzulo anthu onse amene ankakhala mʼzigwa.