1 Mbiri 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Awa ndi amene anawoloka mtsinje wa Yorodano+ m’mwezi woyamba* pamene mtsinjewo unasefukira mbali zake zonse.+ Kenako anathamangitsira kum’mawa ndi kumadzulo anthu onse amene anali kukhala m’zigwa.
15 Awa ndi amene anawoloka mtsinje wa Yorodano+ m’mwezi woyamba* pamene mtsinjewo unasefukira mbali zake zonse.+ Kenako anathamangitsira kum’mawa ndi kumadzulo anthu onse amene anali kukhala m’zigwa.