2 Mbiri 32:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komabe, Hezekiya anadzichepetsa+ pambuyo pa kudzikuza kwa mtima wake. Anadzichepetsa limodzi ndi anthu a ku Yerusalemu, ndipo mkwiyo wa Yehova sunawagwere m’masiku a Hezekiya.+ Luka 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndithu ndikukuuzani, Munthu ameneyu anapita kwawo ataonedwa kukhala wolungama kwambiri+ kusiyana ndi wina uja, chifukwa aliyense wodzikweza adzam’nyazitsa, koma wodzichepetsa adzamukweza.”+ 1 Petulo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho dzichepetseni pansi pa dzanja lamphamvu la Mulungu, kuti adzakukwezeni m’nthawi yake.+
26 Komabe, Hezekiya anadzichepetsa+ pambuyo pa kudzikuza kwa mtima wake. Anadzichepetsa limodzi ndi anthu a ku Yerusalemu, ndipo mkwiyo wa Yehova sunawagwere m’masiku a Hezekiya.+
14 Ndithu ndikukuuzani, Munthu ameneyu anapita kwawo ataonedwa kukhala wolungama kwambiri+ kusiyana ndi wina uja, chifukwa aliyense wodzikweza adzam’nyazitsa, koma wodzichepetsa adzamukweza.”+