27 chifukwa chakuti mtima wako+ unali wofewa ndipo unadzichepetsa+ chifukwa cha Mulungu utamva mawu ake okhudza malo ano ndi anthu ake, ndipo unadzichepetsa pamaso panga+ n’kung’amba+ zovala zako ndi kulira pamaso panga, ineyo ndamva,+ ndiwo mawu a Yehova.