2 Mbiri 32:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komabe, Hezekiya anadzichepetsa+ pambuyo pa kudzikuza kwa mtima wake. Anadzichepetsa limodzi ndi anthu a ku Yerusalemu, ndipo mkwiyo wa Yehova sunawagwere m’masiku a Hezekiya.+
26 Komabe, Hezekiya anadzichepetsa+ pambuyo pa kudzikuza kwa mtima wake. Anadzichepetsa limodzi ndi anthu a ku Yerusalemu, ndipo mkwiyo wa Yehova sunawagwere m’masiku a Hezekiya.+