2 Mafumu 20:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo Hezekiya anauza Yesaya kuti: “Mawu a Yehova amene mwalankhulawa ndi abwino.”+ Anapitiriza kuti: “Ngati mtendere ndi chilungamo+ zipitirire m’masiku anga, ndiye kuti zili bwino, si choncho?”+
19 Pamenepo Hezekiya anauza Yesaya kuti: “Mawu a Yehova amene mwalankhulawa ndi abwino.”+ Anapitiriza kuti: “Ngati mtendere ndi chilungamo+ zipitirire m’masiku anga, ndiye kuti zili bwino, si choncho?”+